Danieli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinamva dzanja la munthu likundikhudza,+ ndipo linayamba kundigwedeza pang’onopang’ono n’kundidzutsa. Nditadzuka ndinagwada ndi kugwira pansi ndi manja anga. Zekariya 4:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anabwerera n’kundidzutsa, ndipo ndinadzuka ngati munthu amene anali kugona.+
10 Pamenepo ndinamva dzanja la munthu likundikhudza,+ ndipo linayamba kundigwedeza pang’onopang’ono n’kundidzutsa. Nditadzuka ndinagwada ndi kugwira pansi ndi manja anga.
4 Mngelo amene anali kulankhula ndi ine uja anabwerera n’kundidzutsa, ndipo ndinadzuka ngati munthu amene anali kugona.+