Danieli 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Inapitiriza kukula mpaka inafika kwa khamu lakumwamba,+ moti inachititsa ena mwa khamuli ndi nyenyezi zina+ kugwera padziko lapansi ndipo inazipondaponda.+ Chivumbulutso 13:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ngati wina akuyenera kutengedwa ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko.+ Ngati wina adzapha ndi lupanga, adzaphedwa ndi lupanga.+ Apa m’pamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+ Chivumbulutso 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+
10 Inapitiriza kukula mpaka inafika kwa khamu lakumwamba,+ moti inachititsa ena mwa khamuli ndi nyenyezi zina+ kugwera padziko lapansi ndipo inazipondaponda.+
10 Ngati wina akuyenera kutengedwa ukapolo, adzapitadi ku ukapoloko.+ Ngati wina adzapha ndi lupanga, adzaphedwa ndi lupanga.+ Apa m’pamene oyera+ akufunika kupirira+ ndiponso kukhala ndi chikhulupiriro.+
6 pakuti iwo anakhetsa magazi a oyera ndi a aneneri.+ Ndipo inu mwawapatsa magazi+ kuti amwe, ndipo n’zowayenereradi.”+