Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+ Chivumbulutso 22:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Anandiuzanso kuti: “Usatsekere mawu a ulosi a mumpukutu uwu, pakuti nthawi yoikidwiratu yayandikira.+
14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
10 Anandiuzanso kuti: “Usatsekere mawu a ulosi a mumpukutu uwu, pakuti nthawi yoikidwiratu yayandikira.+