Chivumbulutso 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Wodala+ ndi munthu amene amawerenga mokweza,+ ndiponso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu,+ komanso amene akusunga zolembedwamo,+ pakuti nthawi yoikidwiratu ili pafupi.+
3 Wodala+ ndi munthu amene amawerenga mokweza,+ ndiponso anthu amene akumva mawu a ulosi umenewu,+ komanso amene akusunga zolembedwamo,+ pakuti nthawi yoikidwiratu ili pafupi.+