Danieli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Atafika, ndinachita mantha ndipo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ dziwa+ kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi ya mapeto.”+
17 Chotero iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Atafika, ndinachita mantha ndipo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ dziwa+ kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi ya mapeto.”+