Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+ Danieli 12:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo utseke ndi kumata bukuli+ kufikira nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzayenda uku ndi uku ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+ Danieli 12:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+
14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
4 “Koma iwe Danieli, sunga mawuwa mwachinsinsi ndipo utseke ndi kumata bukuli+ kufikira nthawi yamapeto.+ Anthu ambiri adzayenda uku ndi uku ndipo adzadziwa zinthu zambiri zoona.”+
9 Iye anandiyankha kuti: “Pita Danieli, pakuti mawuwa asungidwa mwachinsinsi ndipo atsekedwa ndi kumatidwa kufikira nthawi yamapeto.+