Yeremiya 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+ Yeremiya 29:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwanira muli ku Babulo ndidzakucheukirani anthu inu,+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa lokubwezeretsani kumalo ano.’+ Zekariya 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+
11 Dziko lonseli lidzakhala bwinja, chinthu chodabwitsa, ndipo mitundu imeneyi idzatumikira mfumu ya ku Babulo zaka 70.”’+
10 “Yehova wanena kuti, ‘Zaka 70 zikadzakwanira muli ku Babulo ndidzakucheukirani anthu inu,+ ndipo ndidzakwaniritsa lonjezo langa lokubwezeretsani kumalo ano.’+
5 “Kauze anthu onse a m’dzikoli ndi ansembe kuti, ‘Pamene munali kusala kudya+ ndi kulira m’mwezi wachisanu komanso m’mwezi wa 7+ kwa zaka 70,+ kodi munalidi kusala kudya chifukwa cha ine?+