Ekisodo 34:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+ Salimo 40:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+
6 Ndipo Yehova anadutsa pamaso pa Mose akulengeza kuti: “Yehova, Yehova, Mulungu wachifundo+ ndi wachisomo,+ wosakwiya msanga+ ndiponso wodzaza ndi kukoma mtima kosatha+ ndi choonadi.+
11 Inu Yehova, musasiye kundimvera chisoni.+Kukoma mtima kwanu kosatha komanso choonadi chanu zinditeteze nthawi zonse.+