Yesaya 63:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kwanthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo, ngati anthu amene sanatchedwepo ndi dzina lanu.+ Yeremiya 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wothedwa nzeru ndiponso ngati munthu wamphamvu amene sangathe kupulumutsa anthu ake?+ Komatu inu Yehova muli pakati pathu,+ ndipo ife tatchedwa ndi dzina lanu.+ Musatisiye.
19 Kwanthawi yaitali, takhala ngati anthu amene simunawalamulirepo, ngati anthu amene sanatchedwepo ndi dzina lanu.+
9 N’chifukwa chiyani mukukhala ngati munthu wothedwa nzeru ndiponso ngati munthu wamphamvu amene sangathe kupulumutsa anthu ake?+ Komatu inu Yehova muli pakati pathu,+ ndipo ife tatchedwa ndi dzina lanu.+ Musatisiye.