Nehemiya 6:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Patapita nthawi, ntchito yomanga mpanda+ inatha pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli.* Ntchitoyi inatenga masiku 52.
15 Patapita nthawi, ntchito yomanga mpanda+ inatha pa tsiku la 25 la mwezi wa Eluli.* Ntchitoyi inatenga masiku 52.