1 Mbiri 29:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu. Salimo 34:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Ndidzatamanda Yehova nthawi zonse.+Ndidzamutamanda ndi pakamwa panga mosalekeza.+ Salimo 72:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Adalitsike Yehova Mulungu, Mulungu wa Isiraeli,+Iye yekha amene akuchita ntchito zodabwitsa.+ Salimo 113:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Dzina la Yehova lidalitsike,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+
20 Kenako Davide anauza mpingo wonse kuti:+ “Tsopano tamandani+ Yehova Mulungu wanu!” Choncho mpingo wonse unayamba kutamanda Yehova Mulungu wa makolo awo, ndipo anagwada+ n’kuwerama mpaka nkhope zawo pansi+ kwa Yehova ndi kwa mfumu.