1 Mbiri 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+ Yobu 12:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Iye ali ndi nzeru ndi mphamvu.+Amapereka malangizo ndipo amamvetsa zinthu.+ Salimo 147:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye wathu ndi wamkulu ndipo ali ndi mphamvu zochuluka.+Nzeru zake zilibe malire.+ Yeremiya 32:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+
11 Inu Yehova, ukulu,+ mphamvu,+ kukongola,+ ulemerero,+ ndi ulemu+ ndi zanu, chifukwa zinthu zonse zakumwamba ndi za padziko lapansi ndi zanu.+ Ufumu+ ndi wanu, inu Yehova, ndinunso Wokwezeka monga mutu pa onse.+
18 Inu mumasonyeza anthu masauzande ambiri kukoma mtima kosatha.+ Mumabwezera zolakwa za abambo kwa ana awo.*+ Inu ndinu Mulungu woona, wamkulu+ ndi wamphamvu,+ ndipo dzina lanu+ ndinu Yehova wa makamu.+