Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  4 Iye ali ndi mtima wanzeru ndiponso mphamvu zambiri.+

      Ndani angachite naye makani,* koma osavulala?+

  • Yobu 36:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  5 Mulungutu ndi wamphamvu+ ndipo sadzakana munthu.

      Iye ali ndi mphamvu zazikulu zomvetsa zinthu.

  • Yesaya 44:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndimalepheretsa zizindikiro za anthu olankhula zinthu zopanda pake, ndipo ndine amene ndimachititsa olosera kuchita zamisala.+ Ndine amene ndimachititsa anthu anzeru kubwerera kumbuyo, ndiponso amene ndimachititsa nzeru zawo kukhala zopusa.+

  • Danieli 2:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Iye anati: “Dzina la Mulungu likhale lotamandika+ kuyambira kalekale mpaka kalekale, pakuti nzeru ndi mphamvu ndi zake.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena