Danieli 10:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pamenepo ndinamva dzanja la munthu likundikhudza,+ ndipo linayamba kundigwedeza pang’onopang’ono n’kundidzutsa. Nditadzuka ndinagwada ndi kugwira pansi ndi manja anga.
10 Pamenepo ndinamva dzanja la munthu likundikhudza,+ ndipo linayamba kundigwedeza pang’onopang’ono n’kundidzutsa. Nditadzuka ndinagwada ndi kugwira pansi ndi manja anga.