Danieli 5:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 ndipo Dariyo+ Mmedi anapatsidwa ufumuwo ali ndi zaka pafupifupi 62. Danieli 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+
9 M’chaka choyamba cha Dariyo mwana wa Ahasiwero,+ wa mtundu wa Amedi,+ amene anaikidwa kukhala mfumu ya ufumu wa Akasidi,+