2 Mbiri 20:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+
3 Yehosafati atamva zimenezi anachita mantha+ ndipo anatsimikiza mumtima mwake kuti afunefune Yehova.+ Choncho analengeza kuti Ayuda onse asale kudya.+