Salimo 27:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+ Salimo 37:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Pakuti manja a anthu oipa adzathyoledwa,+Koma Yehova adzathandiza anthu olungama.+ Salimo 37:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Koma anafa ndipo sanapezekenso.+Ndinamufunafuna ndipo sindinamupeze.+
2 Anthu ochita zoipa atandiyandikira kuti adye mnofu wanga,+Popeza kuti iwo ndi ondiukira komanso adani anga,+Anapunthwa ndi kugwa.+