Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 12:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  8 Anthu oipa akuyendayenda ponseponse,

      Chifukwa ana a anthu amayamikira zoipa.+

  • Luka 2:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Tsopano m’masiku amenewo, Kaisara Augusito analamula+ kuti anthu onse m’dzikolo akalembetse m’kaundula.

  • Luka 3:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 M’chaka cha 15 cha ulamuliro wa Kaisara Tiberiyo, Pontiyo Pilato anali bwanamkubwa wa Yudeya. Herode*+ anali wolamulira chigawo cha Galileya. Filipo m’bale wake anali wolamulira chigawo cha madera a Itureya ndi Tirakoniti. Ndipo Lusaniyo anali wolamulira chigawo cha Abilene.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena