Luka 18:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku? Chivumbulutso 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze. Chivumbulutso 12:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma dziko lapansi linathandiza mkaziyo.+ Dzikolo linatsegula pakamwa pake ndi kumeza mtsinje umene chinjoka chija chinalavula kuchokera m’kamwa mwake.
7 Ndithu, ngakhale kuti Mulungu amalezera mtima+ osankhidwa ake, kodi sadzaonetsetsa kuti chilungamo+ chachitika kwa iwo, amene amafuulira kwa iye usana ndi usiku?
15 N’chifukwa chake ali pamaso+ pa mpando wachifumu wa Mulungu. Iwo akumuchitira utumiki wopatulika+ usana ndi usiku m’kachisi wake, ndipo wokhala pampando wachifumuyo+ adzatambasulira hema+ wake pamwamba pawo kuti awateteze.
16 Koma dziko lapansi linathandiza mkaziyo.+ Dzikolo linatsegula pakamwa pake ndi kumeza mtsinje umene chinjoka chija chinalavula kuchokera m’kamwa mwake.