Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  9 Pakuti m’kamwa mwawo simutuluka mawu okhulupirika.+

      Mitima yawo yadzaza ndi zinthu zoipa.+

      Mmero wawo ndi manda otseguka.+

      Iwo amalankhula ndi lilime lachinyengo.+

  • Mateyu 7:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 “Chenjerani ndi aneneri onyenga+ amene amabwera kwa inu atavala ngati nkhosa,+ koma mkati mwawo ali mimbulu yolusa.+

  • Machitidwe 20:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndikudziwa kuti ine ndikachoka, mimbulu+ yopondereza idzafika pakati panu ndipo sidzasamalira gulu la nkhosa mwachikondi.

  • Agalatiya 1:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kodi ndiye kuti tsopano ndikufuna kukopa anthu kapena Mulungu? Kapena kodi ndikungofuna kukondweretsa anthu?+ Ndikanakhala kuti ndikukondweretsabe anthu,+ sindikanakhala kapolo wa Khristu.+

  • 2 Petulo 2:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Komanso chifukwa chosirira mwansanje, adzakudyerani masuku pamutu ndi mawu achinyengo.+ Koma chiweruzo chawo chimene chinagamulidwa kalekale+ chikubwera mofulumira, ndipo chiwonongeko chawo sichikuzengereza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena