Mateyu 25:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Ndipo iwowa adzachoka kupita ku chiwonongeko chotheratu,+ koma olungama ku moyo wosatha.”+ Yohane 5:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+ Yohane 6:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Pakuti chifuniro cha Atate wanga ndi chakuti, aliyense woona Mwana ndi kukhulupirira mwa iye akhale nawo moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa pa tsiku lomaliza.”+
29 ndipo adzatuluka. Amene anali kuchita zabwino adzauka kuti alandire moyo.+ Amene anali kuchita zoipa adzauka kuti aweruzidwe.+
40 Pakuti chifuniro cha Atate wanga ndi chakuti, aliyense woona Mwana ndi kukhulupirira mwa iye akhale nawo moyo wosatha,+ ndipo ine ndidzamuukitsa pa tsiku lomaliza.”+