Danieli 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Anthu ambiri amene agona munthaka adzauka.+ Ena adzalandira moyo wosatha+ koma ena adzalandira chitonzo ndipo adzadedwa mpaka kalekale.+ 2 Petulo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+
2 Anthu ambiri amene agona munthaka adzauka.+ Ena adzalandira moyo wosatha+ koma ena adzalandira chitonzo ndipo adzadedwa mpaka kalekale.+
9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+