Danieli 8:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Zinthu zimene waziona ndiponso zimene zanenedwa zokhudza madzulo ndi m’mawa, n’zoona.+ Koma iweyo usunge chinsinsi cha masomphenyawo, chifukwa ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+ Chivumbulutso 10:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano mabingu 7 aja atalankhula, ndinafuna kulemba. Koma ndinamva mawu kumwamba+ akuti: “Tsekera zimene+ mabingu 7 amenewo alankhula, usazilembe.”
26 “Zinthu zimene waziona ndiponso zimene zanenedwa zokhudza madzulo ndi m’mawa, n’zoona.+ Koma iweyo usunge chinsinsi cha masomphenyawo, chifukwa ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
4 Tsopano mabingu 7 aja atalankhula, ndinafuna kulemba. Koma ndinamva mawu kumwamba+ akuti: “Tsekera zimene+ mabingu 7 amenewo alankhula, usazilembe.”