Danieli 8:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Chotero iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Atafika, ndinachita mantha ndipo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ dziwa+ kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi ya mapeto.”+ Danieli 10:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+
17 Chotero iye anabwera pafupi ndi pamene ine ndinaima. Atafika, ndinachita mantha ndipo ndinagwada n’kuwerama mpaka nkhope yanga pansi. Ndiyeno anandiuza kuti: “Iwe mwana wa munthu,+ dziwa+ kuti masomphenyawa ndi okhudza nthawi ya mapeto.”+
14 Tsopano ndabwera kudzakuthandiza kuzindikira zimene zidzagwera anthu a mtundu wako+ m’masiku otsiriza,+ chifukwa masomphenyawa+ ndi okhudza masiku am’tsogolo.”+