Salimo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+ Chivumbulutso 20:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kenako ndinaona mpando wachifumu waukulu woyera, ndi amene anakhalapo.+ Dziko lapansi ndi kumwamba zinathawa+ pamaso pake, ndipo malo a zimenezi sanapezekenso.
10 Patsala kanthawi kochepa, woipa sadzakhalakonso.+Udzayang’ana pamene anali kukhala, ndipo sadzapezekapo.+
11 Kenako ndinaona mpando wachifumu waukulu woyera, ndi amene anakhalapo.+ Dziko lapansi ndi kumwamba zinathawa+ pamaso pake, ndipo malo a zimenezi sanapezekenso.