Danieli 2:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+
23 Ndikukutamandani ndi kukuyamikani,+ inu Mulungu wa makolo anga, chifukwa mwandipatsa nzeru+ ndi mphamvu. Tsopano mwandiuza zimene tinakupemphani, pakuti mwatidziwitsa zimene mfumu inali kufuna.”+