Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsoka kwa chisoti chaulemerero cha zidakwa za ku Efuraimu!+ Chisoticho changokhala ngati nkhata yamaluwa yokongola, imene maluwa ake akufota. Nkhata yamaluwayo yavalidwa ndi mzinda umene uli paphiri, pamwamba pa chigwa chachonde, kumene zidakwa zoledzera ndi vinyozo zimakhala.

  • Mika 6:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Anthu inu mukutsatira zochita za Omuri.+ Zochita zonse za anthu a nyumba ya Ahabu, inunso mukuzichita+ ndipo mukuyendera maganizo awo.+ Pa chifukwa chimenechi ndidzakusandutsani chinthu chodabwitsa ndipo anthu a mumzindawo adzakhala oyenera kuwaimbira mluzu.+ Inuyo mudzatonzedwa ndi mitundu ina ya anthu.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena