Salimo 94:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Wodala ndi munthu wamphamvu amene inu Ya mumamudzudzula,+Komanso amene inu mumamuphunzitsa chilamulo chanu,+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
12 Wodala ndi munthu wamphamvu amene inu Ya mumamudzudzula,+Komanso amene inu mumamuphunzitsa chilamulo chanu,+ Aheberi 12:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+
6 Pakuti Yehova amalanga aliyense amene iye amamukonda, ndipo amakwapula aliyense amene iye amamulandira monga mwana wake.”+