Hoseya 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+ Hoseya 13:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndiyeno ndinakupatsa mfumu nditakwiya+ ndipo ndidzaichotsa nditakwiya.+
4 Ziyenera kukhala choncho chifukwa chakuti kwa masiku ambiri, ana a Isiraeli adzakhala opanda mfumu,+ kalonga, nsembe,+ chipilala chopatulika, efodi,+ ndi aterafi.*+