Yeremiya 2:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+ Yeremiya 48:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+ Ezekieli 36:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Dziwani kuti ine sindidzachita zimenezi chifukwa cha inu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Inu a nyumba ya Isiraeli, chitani manyazi ndi kuona kuti mwanyozeka chifukwa cha njira zanu.’+
26 “Monga mmene mbala imachitira manyazi ikagwidwa, anthu a m’nyumba ya Isiraeli nawonso achita manyazi,+ iwowo, mafumu awo, akalonga awo, ansembe awo ndiponso aneneri awo.+
13 Amowabuwo adzachita manyazi ndi Kemosi,+ monga mmene anthu a m’nyumba ya Isiraeli achitira manyazi ndi Beteli, mzinda umene anali kuudalira.+
32 Dziwani kuti ine sindidzachita zimenezi chifukwa cha inu,’+ watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa. ‘Inu a nyumba ya Isiraeli, chitani manyazi ndi kuona kuti mwanyozeka chifukwa cha njira zanu.’+