Yobu 38:41 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya? Salimo 104:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mkango wamphamvu umabangula pofunafuna nyama,+Ndiponso popempha chakudya kwa Mulungu.+ Salimo 145:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+ Salimo 147:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye amapatsa zilombo chakudya chawo,+Amapatsanso ana a makwangwala chakudya chimene amalirira.+
41 Ndani amakonzera khwangwala chakudya,+Ana ake akamalirira Mulungu kuti awathandize,Akamadzandira chifukwa chosowa chakudya?
15 Zolengedwa zonse zimayang’ana kwa inu mwachiyembekezo,+Ndipo mumazipatsa chakudya pa nyengo yake.+