Chivumbulutso 9:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pachifuwa pawo panali zotetezera+ zokhala ngati zachitsulo. Ndipo phokoso la mapiko awo linali ngati phokoso la magaleta+ okokedwa ndi mahatchi ambiri omwe akuthamangira kunkhondo.+
9 Pachifuwa pawo panali zotetezera+ zokhala ngati zachitsulo. Ndipo phokoso la mapiko awo linali ngati phokoso la magaleta+ okokedwa ndi mahatchi ambiri omwe akuthamangira kunkhondo.+