Yoweli 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Amadumphadumpha ndipo amachita mkokomo ngati magaleta oyenda pamwamba pa mapiri+ ndiponso ngati moto walawilawi umene ukutentha mapesi.+ Iwo ali ngati anthu amphamvu amene afola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+
5 Amadumphadumpha ndipo amachita mkokomo ngati magaleta oyenda pamwamba pa mapiri+ ndiponso ngati moto walawilawi umene ukutentha mapesi.+ Iwo ali ngati anthu amphamvu amene afola mwa dongosolo lomenyera nkhondo.+