Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yesaya 28:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsoka kwa chisoti chaulemerero cha zidakwa za ku Efuraimu!+ Chisoticho changokhala ngati nkhata yamaluwa yokongola, imene maluwa ake akufota. Nkhata yamaluwayo yavalidwa ndi mzinda umene uli paphiri, pamwamba pa chigwa chachonde, kumene zidakwa zoledzera ndi vinyozo zimakhala.

  • Amosi 6:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Inu mukumwera vinyo m’makapu akuluakulu+ ndipo mukudzola mafuta apamwamba kwambiri+ komanso simunamve ululu pamene tsoka linagwera Yosefe.+

  • Luka 21:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 “Koma samalani kuti mitima yanu isalemedwe ndi kudya kwambiri, kumwa kwambiri,+ ndi nkhawa+ za moyo, kuti tsikulo lingadzakufikireni modzidzimutsa+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena