Yeremiya 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pachifukwa chimenechi valani ziguduli,* anthu inu.+ Dzigugudeni pachifuwa ndi kulira mofuula,+ chifukwa mkwiyo woyaka moto wa Yehova sunatichokere.+ Yakobo 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tamverani tsopano inu anthu achuma.+ Lirani, fuulani chifukwa cha masautso amene akubwera kwa inu.+
8 Pachifukwa chimenechi valani ziguduli,* anthu inu.+ Dzigugudeni pachifuwa ndi kulira mofuula,+ chifukwa mkwiyo woyaka moto wa Yehova sunatichokere.+
5 Tamverani tsopano inu anthu achuma.+ Lirani, fuulani chifukwa cha masautso amene akubwera kwa inu.+