Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezara 10:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Tsopano Ezara atangomaliza kupemphera+ ndi kuvomereza machimo,+ komwe ankachita akulira ndiponso ali chogona+ patsogolo pa nyumba+ ya Mulungu woona, Aisiraeli anasonkhana kwa iye. Iwo anali mpingo waukulu kwambiri, amuna, akazi ndi ana, ndipo anali atalira kwambiri.

  • Yesaya 22:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 “M’tsiku limenelo, Yehova wa makamu, Ambuye Wamkulu Koposa,+ adzalamula anthu kuti alire,+ agwetse misozi, amete mipala ndiponso avale ziguduli m’chiuno.+

  • Yakobo 4:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Imvani chisoni ndipo lirani.+ Kuseka kwanu kusanduke kulira, ndipo chisangalalo chanu chisanduke chisoni.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena