Deuteronomo 29:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 ana anu, akazi anu,+ alendo+ okhala mkati mwa msasa wanu, kuyambira wokutolerani nkhuni mpaka wokutungirani madzi,+ Deuteronomo 31:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi. 2 Mbiri 20:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Nthawi yonseyi anthu onse a ku Yuda anali ataimirira pamaso pa Yehova,+ kuphatikizapo akazi awo ndi ana awo, ngakhalenso ana awo ang’onoang’ono.+
11 ana anu, akazi anu,+ alendo+ okhala mkati mwa msasa wanu, kuyambira wokutolerani nkhuni mpaka wokutungirani madzi,+
12 Sonkhanitsani anthu,+ amuna, akazi, ana ndi alendo okhala m’mizinda yanu, kuti amvetsere ndi kuphunzira,+ pakuti ayenera kuopa Yehova Mulungu wanu+ ndi kutsatira mosamala mawu onse a m’chilamulo ichi.
13 Nthawi yonseyi anthu onse a ku Yuda anali ataimirira pamaso pa Yehova,+ kuphatikizapo akazi awo ndi ana awo, ngakhalenso ana awo ang’onoang’ono.+