2 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapereka nsembe yopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+ Mateyu 23:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 kuti magazi onse olungama okhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu,+ kuyambira magazi a Abele+ wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+
12 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapereka nsembe yopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+
35 kuti magazi onse olungama okhetsedwa padziko lapansi abwere pa inu,+ kuyambira magazi a Abele+ wolungama+ mpaka magazi a Zekariya mwana wa Barakiya, amene inu munamupha pakati pa nyumba yopatulika ndi guwa lansembe.+