Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 34:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Ndidzasamalira nkhosa zanga ngati mmene amachitira munthu amene amadyetsa gulu la nkhosa+ zake pamene ali pakati pa nkhosa zimene zinabalalika.+ Pa tsiku la mitambo ndi mdima wandiweyani, ndidzapulumutsa nkhosazo kuchokera m’malo onse kumene zinabalalikira.+

  • Chivumbulutso 16:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mngelo wachisanu anathira mbale yake pampando wachifumu wa chilombo.+ Pamenepo ufumu wake unachita mdima,+ ndipo anthu anayamba kudziluma malilime chifukwa cha ululu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena