Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ Salimo 115:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Amene amawapanga adzafanana nawo.+Onse amene amawakhulupirira adzakhala ngati mafanowo.+ Machitidwe 7:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Inutu munali kunyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi+ ya mulungu Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Chotero ndidzakupitikitsirani+ kutali kupitirira Babulo.’
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
43 Inutu munali kunyamula chihema cha Moloki+ ndi nyenyezi+ ya mulungu Refani, mafano amene munapanga kuti muziwalambira. Chotero ndidzakupitikitsirani+ kutali kupitirira Babulo.’