2 Mafumu 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+ Amosi 3:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”
9 Iye anatentha nyumba ya Yehova,+ nyumba ya mfumu,+ nyumba zonse za mu Yerusalemu,+ ndi nyumba ya munthu aliyense wotchuka.+
15 Nyumba yokhalamo m’nyengo yozizira+ ndi nyumba yokhalamo m’nyengo yotentha+ ndidzazigwetsa.’ “‘Nyumba zaminyanga ya njovu zidzafafanizidwa+ ndipo nyumba zambiri zidzawonongedwa,’+ watero Yehova.”