Amosi 5:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+ Amosi 6:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha.
5 Musakhale ndi mtima wofuna kupita ku Beteli+ ndipo musabwere ku Giligala.+ Musadutse malire kupita ku Beere-seba+ chifukwa ndithu Giligala adzagwidwa ndi kutengedwa kupita ku ukapolo+ ndipo Beteli adzakhala malo ochitikira zinthu zamatsenga.+
7 “Anthu amenewa adzakhala oyambirira kupita ku ukapolo,+ ndipo phwando laphokoso la anthu ogona modziwongola pamabedi lidzatha.