Deuteronomo 32:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+ Mika 2:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Anthu inu musalosere.+ Aneneri amalosera koma sadzalosera zokhudza tsoka limeneli. Ndithu zochititsa manyazi zidzawagwera.+
2 Malangizo anga adzagwa ngati mvula,+Mawu anga adzatsika ngati mame,+Ngati mvula yowaza pa udzu,+Ngatinso mvula yamphamvu pazomera.+
6 Anthu inu musalosere.+ Aneneri amalosera koma sadzalosera zokhudza tsoka limeneli. Ndithu zochititsa manyazi zidzawagwera.+