Deuteronomo 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno ndinakuuzani kuti, ‘Mwafika m’dera lamapiri la Aamori, limene Yehova Mulungu wathu akutipatsa.+
20 Ndiyeno ndinakuuzani kuti, ‘Mwafika m’dera lamapiri la Aamori, limene Yehova Mulungu wathu akutipatsa.+