Numeri 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Munthu aliyense, mwamuna kapena mkazi, akachita lonjezo lapadera lokhala Mnaziri+ kwa Yehova, Oweruza 13:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+ Maliro 4:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+
2 “Lankhula ndi ana a Isiraeli, ndipo uwauze kuti, ‘Munthu aliyense, mwamuna kapena mkazi, akachita lonjezo lapadera lokhala Mnaziri+ kwa Yehova,
5 Pakuti udzatenga pakati ndi kubereka mwana wamwamuna. M’mutu mwake musadzadutse lezala+ chifukwa mwanayo adzakhala Mnaziri+ wa Mulungu potuluka m’mimba.+ Iye adzakhala patsogolo populumutsa Isiraeli m’manja mwa Afilisiti.”+
7 Anaziri+ ake anali oyera kuposa chipale chofewa.+ Analinso oyera kuposa mkaka.Ndipotu anali ofiira+ kuposa miyala yamtengo wapatali ya korali. Analinso osalala ngati mwala wa safiro.+