Yeremiya 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+ Maliro 1:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+ Ezekieli 23:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 “Choncho iwe Oholiba, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndichititsa kuti amuna amene anali zibwenzi zako akuukire.+ Amenewa ndi amuna amene unawasiya chifukwa chonyansidwa nawo. Ine ndidzawabweretsa kuti akuukire kuchokera kumbali zonse.+
6 Tsopano ndapereka mayiko onsewa m’manja mwa mtumiki wanga+ Nebukadinezara, mfumu ya Babulo.+ Ndamupatsanso nyama zakutchire kuti zimutumikire.+
19 Ndaitana anthu ondikonda kwambiri,+ koma anthuwo andichitira zachinyengo.Ansembe anga ndiponso akuluakulu atha+ mumzinda.Atha pamene anali kufunafuna chakudya choti adye kuti adzitsitsimutse.+
22 “Choncho iwe Oholiba, Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Ndichititsa kuti amuna amene anali zibwenzi zako akuukire.+ Amenewa ndi amuna amene unawasiya chifukwa chonyansidwa nawo. Ine ndidzawabweretsa kuti akuukire kuchokera kumbali zonse.+