-
Yeremiya 38:22Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
22 Taonani! Akazi onse amene atsala m’nyumba ya mfumu ya Yuda+ akutuluka nawo panja kupita nawo kwa akalonga a mfumu ya Babulo,+ ndipo akaziwo akunena kuti,
‘Amuna amene unali kukhala nawo pa mtendere akunyengerera+ ndipo akugonjetsa.+
Achititsa kuti mapazi ako amire m’matope ndipo iwo abwerera ndipo akusiya.’+
-