Yona 3:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako Yona analowa mumzindawo ndi kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Iye anali kulalikira kuti: “Kwangotsala masiku 40 okha ndipo Nineve awonongedwa.”+
4 Kenako Yona analowa mumzindawo ndi kuyenda ulendo wa tsiku limodzi. Iye anali kulalikira kuti: “Kwangotsala masiku 40 okha ndipo Nineve awonongedwa.”+