Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 39:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo gulu lankhondo la Akasidi linawathamangitsa+ ndipo Zedekiya anamupeza m’chipululu cha Yeriko.+ Atamugwira, anamutenga ndi kupita naye kwa Nebukadirezara mfumu ya Babulo ku Ribila,+ m’dziko la Hamati,+ kuti Nebukadirezara akamuweruze.+

  • Yeremiya 52:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Kenako Akasidiwo anagwira mfumuyo n’kupita nayo ku Ribila,+ kwa mfumu ya Babulo,+ m’dziko la Hamati,+ kuti mfumu ya Babuloyo ikamuweruze.+

  • Danieli 5:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Chifukwa chakuti Mulungu anamupatsa ukulu umenewu, anthu a mitundu yosiyanasiyana, olankhula zinenero zosiyanasiyana anali kunjenjemera ndi kuchita mantha pamaso pake.+ Iye akafuna kupha munthu aliyense anali kumupha, akafuna kuwononga munthu aliyense anali kumuwononga, akafuna kukweza munthu aliyense anali kumukweza ndipo akafuna kutsitsa munthu aliyense anali kumutsitsa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena