Genesis 15:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Koma m’badwo wachinayi udzabwerera kuno,+ chifukwa nthawi yoti Aamori alangidwe sinakwane.”+ Mateyu 23:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Choncho malizitsani ntchito+ imene makolo anu anayamba. 1 Atesalonika 2:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+
16 Akutero pamene akuyesa kutiletsa+ kulankhula kwa anthu a mitundu ina kuti angapulumutsidwe.+ Chotsatira chake n’chakuti, pochita zimenezi nthawi zonse akudzazitsa+ machimo awo. Koma tsopano mkwiyo wake wawafikira.+